Salimo 116:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova,+Inetu ndine mtumiki wanu.+Ndine mtumiki wanu, mwana wa kapolo wanu wamkazi.+Mwamasula zingwe zimene anandimanga nazo.+
16 Inu Yehova,+Inetu ndine mtumiki wanu.+Ndine mtumiki wanu, mwana wa kapolo wanu wamkazi.+Mwamasula zingwe zimene anandimanga nazo.+