Salimo 86:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Patsani mtumiki wanu mphamvu,+Ndipo pulumutsani mwana wa kapolo wanu wamkazi.+ Luka 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno Mariya anati: “Ndinetu kapolo wa Yehova!+ Zimene mwanenazo zichitike ndithu kwa ine.” Pamenepo mngeloyo anamusiya.
16 Ndicheukireni ndi kundikomera mtima.+Patsani mtumiki wanu mphamvu,+Ndipo pulumutsani mwana wa kapolo wanu wamkazi.+
38 Ndiyeno Mariya anati: “Ndinetu kapolo wa Yehova!+ Zimene mwanenazo zichitike ndithu kwa ine.” Pamenepo mngeloyo anamusiya.