Yobu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mahema a anthu olanda amakhala opanda nkhawa,+Ndipo anthu okwiyitsa Mulungu amakhala pa mtendereWofanana ndi wa munthu amene watenga mulungu* m’manja mwake.+ Yobu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyumba zawo zili pa mtendere, zosaopa chilichonse,+Ndipo ndodo ya Mulungu sili pa iwo.
6 Mahema a anthu olanda amakhala opanda nkhawa,+Ndipo anthu okwiyitsa Mulungu amakhala pa mtendereWofanana ndi wa munthu amene watenga mulungu* m’manja mwake.+