Salimo 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa. Salimo 119:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Yehova, inu ndiye cholowa changa.+Ndalonjeza kusunga mawu anu.+ Salimo 142:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinafuula kwa inu kuti mundithandize, inu Yehova.+Ndinanena kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga,+Gawo langa+ m’dziko la amoyo.”+ Maliro 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndiye cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+
5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa.
5 Ndinafuula kwa inu kuti mundithandize, inu Yehova.+Ndinanena kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga,+Gawo langa+ m’dziko la amoyo.”+
24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndiye cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+