Salimo 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa. Salimo 73:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+ Salimo 119:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Yehova, inu ndiye cholowa changa.+Ndalonjeza kusunga mawu anu.+ Maliro 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndiye cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+
5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa.
26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+
24 Ine ndanena kuti: “Yehova ndiye cholowa changa.+ Pa chifukwa chimenechi, ndidzakhala ndi mtima womudikira.”+