Salimo 63:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+ Salimo 119:81 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 Ine ndafooka chifukwa cholakalaka chipulumutso chanu,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+Moyo wanga ukulakalaka inu.+Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inuM’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+