Maliro 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wataya guwa lake lansembe.+ Iye wanyoza malo ake opatulika.+Wapereka m’manja mwa adani makoma* a nsanja zake zokhalamo.+Iwo afuula m’nyumba ya Yehova ngati pa tsiku lachikondwerero.+
7 Yehova wataya guwa lake lansembe.+ Iye wanyoza malo ake opatulika.+Wapereka m’manja mwa adani makoma* a nsanja zake zokhalamo.+Iwo afuula m’nyumba ya Yehova ngati pa tsiku lachikondwerero.+