Salimo 104:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzifunditsa kuwala ngati chofunda,+Mwatambasula kumwamba ngati nsalu ya chihema.+