Salimo 94:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyamukani inu Woweruza dziko lapansi.+Perekani chilango kwa anthu odzikweza.+ Mika 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzanja lanu lidzakhala pamwamba pa adani anu,+ ndipo adani anu onse adzaphedwa.”+