Yobu 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ndinkapulumutsa wosautsika wopempha thandizo,+Ndiponso mwana wamasiye* ndi aliyense amene analibe womuthandiza.+ Miyambo 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pulumutsa anthu amene atengedwa kuti akaphedwe, ndipo amene akudzandira popita ku imfa, chonde uwabweze.+
12 Pakuti ndinkapulumutsa wosautsika wopempha thandizo,+Ndiponso mwana wamasiye* ndi aliyense amene analibe womuthandiza.+
11 Pulumutsa anthu amene atengedwa kuti akaphedwe, ndipo amene akudzandira popita ku imfa, chonde uwabweze.+