Salimo 76:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene Mulungu ananyamuka ndi kupereka chiweruzo,+Kuti apulumutse anthu onse ofatsa padziko lapansi.+ [Seʹlah.] Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
9 Pamene Mulungu ananyamuka ndi kupereka chiweruzo,+Kuti apulumutse anthu onse ofatsa padziko lapansi.+ [Seʹlah.]
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+