Yesaya 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova adzakupatsani masautso kuti akhale chakudya chanu, ndiponso adzakupatsani kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa.+ Koma Mlangizi wako Wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso ako adzayamba kuona Mlangizi wako Wamkulu.+
20 Yehova adzakupatsani masautso kuti akhale chakudya chanu, ndiponso adzakupatsani kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa.+ Koma Mlangizi wako Wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso ako adzayamba kuona Mlangizi wako Wamkulu.+