Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 36:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungutu amachita zinthu zapamwamba ndi mphamvu zake.

      Kodi mphunzitsi winanso ndani wofanana naye?

  • Salimo 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+

      Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+

  • Salimo 71:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+

      Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+

  • Salimo 119:102
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 102 Sindinapatuke pa zigamulo zanu,+

      Pakuti inu mwandilangiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena