2 Mbiri 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iweyo ukayenda pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, mwa kuchita zonse zimene ndakulamula+ ndi kusunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+ Salimo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zigamulo zake zonse zili pamaso panga,+Ndipo malamulo ake sindidzawataya.+
17 “Iweyo ukayenda pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, mwa kuchita zonse zimene ndakulamula+ ndi kusunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+