Salimo 72:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo. Yesaya 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ntchito ya chilungamo chenicheni idzakhala mtendere,+ ndipo zochita za chilungamo chenicheni zidzakhala bata ndi mtendere mpaka kalekale.+
3 Mapiri atenge mtendere ndi kupita nawo kwa anthu,+Komanso zitunda zitenge mtendere wopezeka mwachilungamo.
17 Ntchito ya chilungamo chenicheni idzakhala mtendere,+ ndipo zochita za chilungamo chenicheni zidzakhala bata ndi mtendere mpaka kalekale.+