Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] Salimo 143:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]
8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+