Salimo 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+ Salimo 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu ali pakati pa mzinda.+ Mzindawo sudzagwedezeka.+Mulungu adzauthandiza m’bandakucha.+ Salimo 59:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu yanu,+M’mawa ndidzanena mosangalala za kukoma mtima kwanu kosatha.+Pakuti inu mwakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya masautso.+
8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+
16 Koma ine, ndidzaimba za mphamvu yanu,+M’mawa ndidzanena mosangalala za kukoma mtima kwanu kosatha.+Pakuti inu mwakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndiponso malo anga othawirako pa nthawi ya masautso.+