Salimo 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sindinakhale pansi pamodzi ndi anthu achinyengo.+Ndipo sindinayanjane ndi anthu obisa umunthu wawo.+ Salimo 69:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+ Miyambo 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Thamangitsa wonyoza, kuti mikangano ithe ndiponso kuti milandu ndi kunyozedwa zilekeke.+ 2 Petulo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+
4 Sindinakhale pansi pamodzi ndi anthu achinyengo.+Ndipo sindinayanjane ndi anthu obisa umunthu wawo.+
12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+
3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+