Salimo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuikiza mzimu* wanga m’manja mwanu.+Mwandiwombola,+ inu Yehova, Mulungu wachoonadi.+ Salimo 130:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+ Salimo 145:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachisomo ndi wachifundo,+Wosakwiya msanga ndi wosonyeza kukoma mtima kosatha komanso kwakukulu.+ Yoweli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+
7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+
8 Yehova ndi wachisomo ndi wachifundo,+Wosakwiya msanga ndi wosonyeza kukoma mtima kosatha komanso kwakukulu.+
13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+