2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu. Salimo 119:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Mkwiyo ukuyaka mumtima mwanga chifukwa cha oipa,+Amene akusiya chilamulo chanu.+ Yeremiya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Yehova anayankha kuti: “Chifukwa chakuti iwo asiya chilamulo changa chimene ndinawapatsa kuti chizikhala pamaso pawo, komanso chifukwa chakuti iwo sanamvere mawu anga ndi kuwatsatira,+
14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu.
13 Ndiyeno Yehova anayankha kuti: “Chifukwa chakuti iwo asiya chilamulo changa chimene ndinawapatsa kuti chizikhala pamaso pawo, komanso chifukwa chakuti iwo sanamvere mawu anga ndi kuwatsatira,+