Salimo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Yehova poimba zeze.+Muimbireni nyimbo zomutamanda ndi choimbira cha zingwe 10.+ Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Aefeso 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse.
23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
20 m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu. Nthawi zonse muziyamika+ Mulungu, Atate wathu, pa zinthu zonse.