Yeremiya 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Abusa achita zinthu mopanda nzeru,+ ndipo sanayese n’komwe kufunafuna Yehova.+ N’chifukwa chake sanachite zinthu mozindikira, ndipo ziweto zawo zonse zabalalika.”+ Yeremiya 50:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Anthu inu munali kusangalala,+ ndipo munali kukondwera pamene munali kulanda cholowa changa.+ Munali kudumphadumpha pamsipu ngati ng’ombe yaikazi yosaberekapo+ ndipo munali kulira ngati mahatchi amphongo.+
21 Abusa achita zinthu mopanda nzeru,+ ndipo sanayese n’komwe kufunafuna Yehova.+ N’chifukwa chake sanachite zinthu mozindikira, ndipo ziweto zawo zonse zabalalika.”+
11 “Anthu inu munali kusangalala,+ ndipo munali kukondwera pamene munali kulanda cholowa changa.+ Munali kudumphadumpha pamsipu ngati ng’ombe yaikazi yosaberekapo+ ndipo munali kulira ngati mahatchi amphongo.+