Yeremiya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pamalo anga odyetsera ziweto!”+ watero Yehova. Ezekieli 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pang’ono ndi pang’ono zinamwazikana chifukwa chakuti zinalibe m’busa.+ Choncho zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire ndipo zinapitiriza kumwazikana.+
23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pamalo anga odyetsera ziweto!”+ watero Yehova.
5 Pang’ono ndi pang’ono zinamwazikana chifukwa chakuti zinalibe m’busa.+ Choncho zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire ndipo zinapitiriza kumwazikana.+