Salimo 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+ Salimo 100:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+Muyamikeni, tamandani dzina lake.+
23 Amene akupereka nsembe yoyamikira kwa ine ndi amene akundilemekeza.+Ndipo amene akuyenda panjirayo motsimikiza,Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+
4 Lowani pazipata zake ndi mawu oyamikira,+Lowani m’mabwalo ake ndi mawu otamanda.+Muyamikeni, tamandani dzina lake.+