Salimo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+ Miyambo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku onse a munthu wosautsika amakhala oipa,+ koma munthu wamtima wosangalala amachita phwando nthawi zonse.+
11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+
15 Masiku onse a munthu wosautsika amakhala oipa,+ koma munthu wamtima wosangalala amachita phwando nthawi zonse.+