Salimo 102:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masiku a moyo wanga ali ngati chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa,+Ndipo ndauma ngati udzu.+ Salimo 143:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga+ walefuka,Ndipo wachita dzanzi.+ Yesaya 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+
11 Masiku a moyo wanga ali ngati chithunzithunzi chimene chimazimiririka dzuwa likalowa,+Ndipo ndauma ngati udzu.+
7 Udzu wobiriwirawo wauma ndipo maluwawo afota+ chifukwa mpweya wa Yehova wauzirapo.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.+