Salimo 77:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndidzakumbukira Mulungu ndipo ndidzavutika maganizo.+Ine ndasautsika. N’chifukwa chake ndafooka.+ [Seʹlah.] Salimo 142:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+
3 Ndidzakumbukira Mulungu ndipo ndidzavutika maganizo.+Ine ndasautsika. N’chifukwa chake ndafooka.+ [Seʹlah.]
3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+