Salimo 77:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikakumbukira Mulungu ndimabuula.+Ndimavutika kwambiri mumtima ndipo mphamvu zanga zimatha.*+ (Selah)
3 Ndikakumbukira Mulungu ndimabuula.+Ndimavutika kwambiri mumtima ndipo mphamvu zanga zimatha.*+ (Selah)