Salimo 142:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+ Salimo 143:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga+ walefuka,Ndipo wachita dzanzi.+
3 Ndinachita zimenezi pamene mtima wanga+ unalefuka.Pamenepo, munadziwa njira yanga.+Adani anga anditchera msampha+M’njira imene ndikuyenda.+