Deuteronomo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+ Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+ Yona 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu okhulupirira mafano, amaleka kusonyeza kukoma mtima kwawo kosatha.+
19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+
7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+