Salimo 89:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+ Salimo 145:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ufumu wanu ndi ufumu umene udzakhalapobe mpaka kalekale.+Ulamuliro wanu udzakhalapobe ku mibadwo yonse.+
11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+
13 Ufumu wanu ndi ufumu umene udzakhalapobe mpaka kalekale.+Ulamuliro wanu udzakhalapobe ku mibadwo yonse.+