Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Aefeso 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+