Yesaya 65:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo adzamanga nyumba n’kukhalamo.+ Adzabzala minda ya mpesa n’kudya zipatso zake.+ Yeremiya 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Mangani nyumba ndi kukhalamo. Limani minda ndi kudya zipatso zake.+