Yesaya 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova walumbira ndi dzanja lake lamanja+ ndiponso ndi mkono wake wamphamvu+ kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu ngati chakudya,+ ndipo alendo sadzamwanso vinyo wanu watsopano+ amene munachita kumuvutikira.
8 Yehova walumbira ndi dzanja lake lamanja+ ndiponso ndi mkono wake wamphamvu+ kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu ngati chakudya,+ ndipo alendo sadzamwanso vinyo wanu watsopano+ amene munachita kumuvutikira.