Genesis 30:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chuma cha Yakobo chinapitirira kuwonjezeka. Iye anakhala ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamila ndi abulu.+ Deuteronomo 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mudzakhala odalitsika mwa anthu onse.+ Pakati panu sipadzapezeka mwamuna, mkazi kapena chiweto chosabereka.+
43 Chuma cha Yakobo chinapitirira kuwonjezeka. Iye anakhala ndi ziweto zambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamila ndi abulu.+
14 Inu mudzakhala odalitsika mwa anthu onse.+ Pakati panu sipadzapezeka mwamuna, mkazi kapena chiweto chosabereka.+