Salimo 138:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 138 Ndidzakutamandani ndi mtima wanga wonse.+Ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani pamaso pa milungu ina.+ Salimo 145:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuti ana a anthu adziwe za ntchito zanu zamphamvu+Ndi kukula kwa ulemerero wa ufumu wanu.+
138 Ndidzakutamandani ndi mtima wanga wonse.+Ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani pamaso pa milungu ina.+