Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Luka 7:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Iwe sunandipsompsone,+ koma chilowereni muno, mayiyu sanaleke kupsompsona mapazi anga mwachikondi. Afilipi 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anachita zimenezi kuti m’dzina la Yesu, onse akumwamba, apadziko lapansi, ndi apansi pa nthaka apinde mawondo awo.+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
45 Iwe sunandipsompsone,+ koma chilowereni muno, mayiyu sanaleke kupsompsona mapazi anga mwachikondi.
10 Anachita zimenezi kuti m’dzina la Yesu, onse akumwamba, apadziko lapansi, ndi apansi pa nthaka apinde mawondo awo.+