1 Akorinto 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale onse akukupatsani moni. Mupatsane moni ndi kupsompsonana kopatulika.+ 1 Petulo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Patsanani moni popsompsonana mwa chikondi chaubale.+ Nonse amene muli ogwirizana ndi Khristu, mtendere ukhale nanu.+
14 Patsanani moni popsompsonana mwa chikondi chaubale.+ Nonse amene muli ogwirizana ndi Khristu, mtendere ukhale nanu.+