Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chonsecho iye wadzaza nyumba zawo ndi zinthu zabwino,+

      Ndipo malangizo a anthu oipa ali kutali ndi ine.+

  • Salimo 144:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nkhokwe zathu ndi zodzaza ndi zakudya zosiyanasiyana.+

      Nkhosa zathu zikuswana kukhala masauzandemasauzande. Nkhosa imodzi ikukhala masauzande 10 m’misewu.

  • Mateyu 5:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake pa anthu oipa ndi abwino, ndi kuvumbitsira mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena