Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+ Salimo 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+Chifukwa cha dzina lanu+ mudzanditsogolera ndi kundilozera njira.+ Yohane 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Komanso, ine sindikhalanso m’dzikoli pakuti ndikubwera kwa inu, koma iwo adakali m’dzikoli.+ Atate Woyera, ayang’anireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi mmene ife tilili.+
11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire cholakwa changa ngakhale kuti n’chachikulu.+
3 Pakuti inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+Chifukwa cha dzina lanu+ mudzanditsogolera ndi kundilozera njira.+
11 “Komanso, ine sindikhalanso m’dzikoli pakuti ndikubwera kwa inu, koma iwo adakali m’dzikoli.+ Atate Woyera, ayang’anireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi mmene ife tilili.+