Salimo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzaimbira Yehova chifukwa wandifupa ndi zinthu zabwino.+ Salimo 119:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndichitireni zabwino, ine mtumiki wanu, kuti ndikhale ndi moyo,+Ndi kuti ndisunge mawu anu.+ Salimo 145:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amayang’anira onse omukonda,+Koma oipa onse adzawafafaniza.+ Aheberi 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+
6 Ndiponso, popanda chikhulupiriro+ n’zosatheka kukondweretsa Mulungu.+ Pakuti aliyense wofika kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti iye alikodi,+ ndi kuti amapereka mphoto+ kwa anthu omufunafuna ndi mtima wonse.+