Salimo 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti nyama iliyonse yakutchire ndi yanga,+Ndiponso nyama zopezeka m’mapiri 1,000.+ 1 Akorinto 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+
20 pakuti munagulidwa pa mtengo wokwera.+ Mulimonse mmene zingakhalire, lemekezani Mulungu+ ndi matupi anu.+