1 Mafumu 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Alozetse mtima wathu+ kwa iye kuti tiyende m’njira zake zonse+ ndi kusunga malamulo ake,+ malangizo ake,+ ndi zigamulo zake,+ zimene analamula makolo athu. Salimo 119:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndilangizeni inu Yehova, kuti ndiyende motsatira malangizo anu,+Kuti nditsatire malangizo anu moyo wanga wonse.+ Salimo 119:124 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 124 Ndichitireni zabwino ine mtumiki wanu monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndipo ndiphunzitseni malamulo anu.+
58 Alozetse mtima wathu+ kwa iye kuti tiyende m’njira zake zonse+ ndi kusunga malamulo ake,+ malangizo ake,+ ndi zigamulo zake,+ zimene analamula makolo athu.
33 Ndilangizeni inu Yehova, kuti ndiyende motsatira malangizo anu,+Kuti nditsatire malangizo anu moyo wanga wonse.+
124 Ndichitireni zabwino ine mtumiki wanu monga mwa kukoma mtima kwanu kosatha,+Ndipo ndiphunzitseni malamulo anu.+