Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 119:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  64 Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kwadzaza dziko lonse lapansi.+

      Ndiphunzitseni malamulo anu.+

  • Yesaya 48:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu, amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,+ amene ndimakuchititsani kuti muyende m’njira imene muyenera kuyendamo.+

  • Yohane 6:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+

  • Yakobo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena