Salimo 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+ Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga+ ndimasangalala kwambiri+ ndi chilamulo cha Mulungu,
2 Koma amakondwera ndi chilamulo cha Yehova,+Ndipo amawerenga ndi kusinkhasinkha chilamulo chake usana ndi usiku.+