Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Salimo 119:97 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Ndimakonda kwambiri chilamulo chanu!+Ndimasinkhasinkha chilamulocho tsiku lonse.+
8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+