Salimo 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Yehova sadzasiya wolungama m’manja mwa woipayo,+Ndipo pamene wolungamayo akuweruzidwa, Mulungu sadzamuona monga wolakwa.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
33 Koma Yehova sadzasiya wolungama m’manja mwa woipayo,+Ndipo pamene wolungamayo akuweruzidwa, Mulungu sadzamuona monga wolakwa.+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+