Salimo 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+ Salimo 119:78 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 78 Odzikuza achite manyazi, chifukwa andisocheretsa popanda chifukwa,+Koma ine ndimasinkhasinkha malamulo anu.+ Hoseya 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’manja mwa wamalonda muli sikelo yachinyengo+ ndipo iye amakonda kuba mwachinyengo.+
11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+
78 Odzikuza achite manyazi, chifukwa andisocheretsa popanda chifukwa,+Koma ine ndimasinkhasinkha malamulo anu.+