Levitiko 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo.+ Musamachite chinyengo poyeza utali wa chinthu, kulemera kwa chinthu+ kapena poyeza zinthu zamadzi. Miyambo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Sikelo yachinyengo imam’nyansa Yehova,+ koma mwala woyezera, wolemera mokwanira, umam’sangalatsa. Amosi 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukunena kuti: ‘Kodi mwezi watsopano utha liti+ kuti tiyambe kugulitsa chakudya?*+ Komanso sabata+ litha liti kuti tiyambe kuchepetsa muyezo wogulitsira zinthu,+ kukweza mtengo ndi kubera wogula mwa kugwiritsa ntchito masikelo achinyengo?+
35 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo.+ Musamachite chinyengo poyeza utali wa chinthu, kulemera kwa chinthu+ kapena poyeza zinthu zamadzi.
5 Inu mukunena kuti: ‘Kodi mwezi watsopano utha liti+ kuti tiyambe kugulitsa chakudya?*+ Komanso sabata+ litha liti kuti tiyambe kuchepetsa muyezo wogulitsira zinthu,+ kukweza mtengo ndi kubera wogula mwa kugwiritsa ntchito masikelo achinyengo?+