Levitiko 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Muzikhala ndi masikelo olondola,+ miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu, muyezo wolondola wa efa ndi muyezo wolondola wa hini.* Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo. Mika 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi m’nyumba ya munthu woipa mukupezekabe chuma chopezedwa mopanda chilungamo,+ ndiponso muyezo woperewera wa efa* umene ndi wosaloleka?
36 Muzikhala ndi masikelo olondola,+ miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu, muyezo wolondola wa efa ndi muyezo wolondola wa hini.* Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.
10 Kodi m’nyumba ya munthu woipa mukupezekabe chuma chopezedwa mopanda chilungamo,+ ndiponso muyezo woperewera wa efa* umene ndi wosaloleka?